Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com
-
0:02 - 0:04Pamene aneneri ndi aphunzitsi a tchalitchi chakale
-
0:04 - 0:08anali kusala kudya ndi kupemphera, Mzimu Woyera unauza Paulo ndi Baranaba
-
0:08 - 0:10kuti ayende ulendo woyamba wa umishonale.
-
0:10 - 0:13Tchalitchi chinawapempherera asananyamuke ulendo wawowo.
-
0:16 - 0:19Iwo anaikidwa manja, ndipo tinawapempherera mochokera pansi pa mtima.
-
0:19 - 0:21Monga tchalitchi chogwirizana, tinawapempherera kuti ayende bwino
-
0:21 - 0:24ndiponso kuti Mulungu awapatse mawu oyenerera
-
0:24 - 0:26oti akayankhule kwa anthu ambirimbiri.
-
0:26 - 0:28Tinapempherera amishonale athuwa kuti zinthu ziwayendere bwino
-
0:28 - 0:30pantchito yawo yofalitsa uthenga wabwino.
-
0:32 - 0:35Paulo ndi Baranaba anayenda kupita kumadera osiyanasiyana.
-
0:35 - 0:38Ku Kupro, analalikira mawu a Mulungu m'masunagoge a Ayuda.
-
0:38 - 0:42Ku Antiyokeya wa ku Pisidiya, pafupifupi anthu onse mumzindawo anasonkhana
-
0:42 - 0:44kuti adzamve mawu a Ambuye.
-
0:44 - 0:46Anthu Amitundu atamva uthenga wawo, anakhulupirira.
-
0:46 - 0:50Mawu a Ambuye anafalikira m'chigawo chonse,
-
0:50 - 0:53ndipo ophunzira anali kusangalala kwambiri komanso anadzazidwa ndi Mzimu Woyera.
-
0:56 - 0:59Paulo ndi Baranaba anaika akulu mu tchalitchi chilichonse
-
0:59 - 1:02ndipo ankasala kudya ndi kuwapempherera powapereka kwa Ambuye.
-
1:02 - 1:05Iwo anasonkhanitsa tchalitchi chonse pamodzi n'kuwauza
-
1:05 - 1:07zonse zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwowo
-
1:07 - 1:10ndiponso mmene anatsegulira khomo la chikhulupiriro kwa anthu Amitundu.
- Title:
- Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com
- Description:
-
The church prayed together before sending them out. www.unitedprayerworks.com
- Video Language:
- English
- Team:
Team Adventist
- Project:
- Artv
- Duration:
- 01:16
![]() |
Cindy Hurlow approved Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
Cindy Hurlow edited Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
Cindy Hurlow accepted Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
Cindy Hurlow edited Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
Darren Bridenbeck (Amara Staff) accepted Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
seventh_day_adventist edited Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
seventh_day_adventist edited Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com | |
![]() |
seventh_day_adventist edited Chewa subtitles for Paul and Barnabas // UnitedPrayerWorks.com |