My names are Britta Natasha Kawinga. I'm a native from eastern part of Zambia. My father is Ngoni and my mother is Nsenga. Dzina langa ndine Britta Kawinga, ndichokera kum'mawa. Ndidzakuimbirakoni kanyimbo ka m'Chichewa Aka kanyimbo koyamba ni kanyimbo kotonthoza mwana ngati alira Ndiponso kanyimbo ndiyankha Uwuuwuwe, uwuwuwe mwana alira, afuna mkaka muperekeni kwa amake akamphikire nkhoto nyemba bwerera iye aa aa eya eya Mwana kalirani njala Mwana kalirani tulo aa eya eya Mwana alira, afuna mkaka muperekeni kwa amake akamphikire nkhoto nyemba bwerera iye aa eya eya mwana kalirani njala mwana kalirani tulo aa eya eya So basically in the Chewa culture when a child is crying, when a child wants to sleep, this is a lullaby that the mother will sing to the child The other one is usually sung when women are pounding. And it goes like this: Titwe, titwe, iyayi titwe, zangalewa Titwe, titwe, iyayi titwe, zangalewa Amayi amfumu, alowa m'sitolo Na muchira wa ng'ombe na mu ndodo kum'manja iii! iii! Titwe, titwe, iyayi, titwe zangalewa Titwe, titwe, iyayi titwe zangalewa Amayi amfumu alowa m'sitolo Na mu mchira wa ng'ombe Na mu ndodo ku m'manja aii! aii! Thank you [m'manja]